Quran Chichewa
Books & Reference Contains ads
Qur'an ya Chichewa free offline.
- Rating
- 4.5
- 26 ratings
- Downloads
- 5K+
- on Google Play
- Price
- Free
- No in-app purchases
- Updated
- Nov 5
- 2019 · v4.3
Screenshots
About Quran Chichewa
Qur'an ya Chichewa offline ikupezeka tsopano pa internet.
Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabic pansi pa Chichewa.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma social media komanso awo omwe sabva Arabic.
Ndipo kwa ma Daiy yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga copy and paste kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Just long click to copy and paste)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.
Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabic pansi pa Chichewa.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma social media komanso awo omwe sabva Arabic.
Ndipo kwa ma Daiy yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga copy and paste kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Just long click to copy and paste)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.
What’s new
Version 4.3 · Updated November 5, 2019
Changed start up color. Removed full screen ads Lowered minimum API level to allow small devices to install the App.
User reviews
Mashaa-Allah!!!. Koma mukanatembenuza kuti Ayat izikhala mmwamba then translation izibwera pansi pake , cos zikumapeleka confusion. Mwina ndi ndekha koma ndi momwe ndikuwonela. Ndilinso ndi chiyembekezo kuti ma Surat enawonso mumaliza kutanthauzira Inshaa-Allah. Timpempha Allah kuti alandile ntchito yanu. Komanso ak...
I'm so proud to be a Muslim and I always thanks Allah for everything.May Allah grant all Muslim Jannah n make it easy for everyone to have this Quran InshaaAllah.
Good work Masha Allah
This is so amazing, may Allah reward abundantly.
Easy to read
Jazakaallah, may Allah reward you inshaallah.
Alternatives to Quran Chichewa
Looking for apps like Quran Chichewa? Here are 4 similar Android apps on Google Play. The highest rated is شات عربي | دردشة وتعارف NeChat (3.8/5), and all 4 are free to download.
-
شات عربي | دردشة وتعارف NeChat 3.8
-
Sketchware Beginners Guide 3.7
-
40 Hadith Nawawi Chichewa and
-
40 Hadith Qudsi in Chichewa
| App | Rating | Price | Installs | Last updated | Compare |
|---|---|---|---|---|---|
| Quran Chichewa | 4.5 / 5 | Free | 5,000+ | Nov 5, 2019 | |
| شات عربي | دردشة وتعارف NeChat | 3.8 / 5 | Free | 50,000+ | May 21, 2020 | Compare |
| Sketchware Beginners Guide | 3.7 / 5 | Free | 10,000+ | May 6, 2021 | Compare |
| 40 Hadith Nawawi Chichewa and | – | Free | 1,000+ | Jan 27, 2019 | Compare |
| 40 Hadith Qudsi in Chichewa | – | Free | 1,000+ | May 6, 2018 | Compare |
Compare Quran Chichewa with the top alternatives: ratings, updates, ASO score and keyword gaps →